Wizzy p
12/03/2026
pano temwa akungotulutsa ma pic uyutu adavaya
12/03/2026
muli mbali iti
USA
IRAN
09/03/2026
komatu guys mmmmhhhh
12/02/2026
ndi angati amene mwasangalala kuchoka kwa zaka pa social media?
16/01/2026
uhule ndi ntima osati mavuto kuli anthu ambili mdziko muno amene akuvutika koma simahule, uyuyu thandizo loyambilila amafunikila kumapemphero k*t chi chiwanda cha uhulecho chikachoke then ndikumuthandiza bwino ku mbali yazachuma koma olo mutamupatsa ndalama zochuluka bwanji popanda mwini wakeyo kulapa kusiya tchimo sangasiye uhule adzikapangabe koma ali ndi ndalama.
07/11/2025
mawu amodzi kwama guys awa
Click here to claim your Sponsored Listing.