KACHA's Blog

KACHA's Blog

Share

14/03/2025

Ndine wokondwa kugawana nanu zaubwino odabwitsa wa Uchi!. Sikuti ndi wo sekemera chabe, komanso ndi wopatsa thanzi.

1. Mphamvu zowonjezera: Uchi umapatsa thupi mphamvu yachilengedwe.
2. Uchi ndi mankhwala achilengedwe akutsokomola, chifuwa ndi zilonda zapakhosi.
3. Kumwa Uchi wodzaza supuni musanagone kumakuthandizani kugona ngati khanda.
4. Kuthandizira kugaya chakudya m'mimba komanso amathandizira thanzi.
5. Uchi umathandiza thupi kudziteteza ND kugonjetsa matenda ena osiyanasiyana.

Mwakonzeka kuyesa Hewe Honey🍯?. Imbani: 0992952906 (Mzuzu).

08/02/2025

GIFTED Design's.

09/12/2024

Click on the link and view the works of Khumbo Ashan Kamoto.

Enter into another World 🌎, read BIRTH OF THE MASK on Google drive.

BIRTH OF THE MASK.pdf

16/08/2024

If your a Graphics Designer, definitely halla my box...

Want your university to be the top-listed University in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Address

Lilongwe

Opening Hours

Monday 07:30 - 20:00
Tuesday 07:30 - 20:00
Wednesday 07:30 - 20:00
Thursday 07:30 - 20:00
Friday 07:30 - 17:00
Saturday 16:30 - 00:30
Sunday 09:00 - 17:00
17:30 - 22:30