Chef Mimi Daka
13/07/2025
Ku induction ceremony ya achimwene ku Kamanzi CCAP, Lilongwe rural west.
Flour 2 cups
Milk 1½ cup
Eggs 3
Sugar 3 tbsp
A pinch of salt
Cooking oil 3 tbsp
Mix them together/muziphatikize zonse pamodzi.
Muzitakase then mutenga pan nkuika pa moto (low heat) nkuikamo timafuta pang'ono nkuthira phalalo.
Video imodzi mmunsimu ikuonetsa mmene mungamalipangire phalalo mu pan, kwinako muzitembenuza kuti zipsye bwinobwino.
Koma pan wake akhale wozolowera mafuta coz sizimafunika phalalo lizimata mu pan.
Prophet ndi yemweyu sitikusintha 😂😂🏃
28/09/2024
Kutatiphe nkutentha komweku 😕
Click here to claim your Sponsored Listing.