RT Solution
18/05/2026
love in tokyo🤣🤣🤣🤣
18/05/2026
Mwazikumbukira ndiwo izi panja zimatchulidwa kuti chani muchiyankhulo chanu ??
18/05/2026
THE CRY OF A BARREN
ndine osabereka. Ndipo anthu akumandiseka. Ena kunditchula mayina, ena akumati ndine othembeleredwa. Koma zenizeni zake nzakuti ineyo ndine osabereka.
Ndinakwatiwapo ndi Mwamuna oyamba emwe ankandikonda ngakhale ndili osabereka. koma achibale ake, anandithamangisa.
Kudzabweranso wina uyu nde anati alibe nthawi yosewelesa.
Achibale anga omwe akumayankhula kuti ndine mbewu yoipa. Kodi ndithawira kuti?
Ena akumati ndinataya mimba zochuluka ndili msikana. Koma zenizeni zake nzakuti' ineyo, osabereka.
Ambuye! Ndine kapolo wanu, invani kulira kwanga. chifukwa inu, muposa osekawo.
follow
18/05/2026
Nthambi yowona za pamsewu m'dziko la South Africa lero yagwira bus yochokera m'dziko muno kupita m'dzikomo ku dera la Limpopo mpomwe linatuta likukumwe lodutsa mlingo omwe imayenera kunyamula.
Malinga ndi nyuzipepala za m'dziko la South Africa, bus'yi imayenera kunyamula anthu 70, koma pomwe anaiyimitsa, inali ndi anthu odutsa 90, zomwe zinapangitsa kuti nthambiyi igwire galimoyoyi.
Izitu zikuchitika patangodutsa sabata imodzi a Malawi ochuluka atafa pa ngozi za pamsewu ziwiri zomwe ina imachoka m'dziko muno kupita ku South Africa pomwe inayo, imachoka ku South Africa kubwera m'dziko muno.
18/05/2026
Zina ukamva🙌🙌
Apolice ku Mponela m'boma la Dowa ,amanga mai wa zaka 53 ,Aliste Adson (maina a chinzungu tu ngati si malawi witu) kamba kogona ndi mwana wa zaka 16
Akuti oganizilidwawo akuganizilidwa kuti anapalamula mlandu umenewu pa 11 may
Shaaa zativuta my gender bola munakapeza wa 18 years apatu basi tu wa ku wire
mwaswela bwanji pamudzi pano?
17/05/2026
🤣
okufa sathokoza 🤦zikomo kwambili ambuye mulungu poti zusa ndimoyo rero ine ndi amene akuwerengayu 🙏
good night ma guys
Ndagwada pasi. Ndikulira mokweza😭 ndikupemphera mobangula kufuna inu Tate muyendele nyengo zathu mdzina la Yesu Khristu 😭😭
Afiti nonse ulemu wanu,ndinu odzichepetsa,odekha, simunajambulitsepo mukukwera ndege,ai zikomo
Click here to claim your Sponsored Listing.