FRESH issues
Munaganiza bwanji ati avula ekha
Follow FRESH issues
Nkhuku ya neba ndiyako yomwe ukaipha mwangozi azagaila akaphika ..12:00 follow FRESH issues for more
Kwa ena likhala lamwai
Kwa ena latsoka
follow FRESH issues
muvezambiri Good morning
Kod mukuziwa kuti nkaka wakhumba umathamdiza bwanji kuti munthu asiye mowa follow FRESH issues for more
Follow FRESH issues
Apolisi ku Lilongwe amanga anthu awiri kaaamba kopezeka ndi minyanga ya njobvu zomwe akuwaganizira kuti amafuna kugulitsa kwa anthu ena ku Likuni my mzindawu.
Wachiwiri kwa mneneri wa a polisi ya Lilongwe a Khumbo Sanyiwa wati anthuwa ndia Gift Phiri a zaka 45 ndi a Florina Lackson a zaka 41.
A Gift Phiri amachokera mmudzi wa Wanyala Mfumu yayikulu Santhe m'boma la Kasungu pomwe a Florina Lackson amachokera mmudzi mwa Chala mdera la Mfumu yaikulu
Click here to claim your Sponsored Listing.