Jesh
Jeeshiiii ๐ฅ๐ฅ๐ฏ
01/11/2025
๐ฅWanga Ndiwe NOW OUT๐ฅ
in All Streaming Platforms
YouTube:
https://youtu.be/jX5c4sLdXuE?si=-mXClSD9KKYo9jUA
Spotify :
https://open.spotify.com/album/1QKMjcT2LEXp9UymbuljeB?utm_campaign=website&utm_medium=Email+&utm_source=SendGrid
Apple Music:
https://music.apple.com/us/album/wanga-ndiwe-single/1847402265
30/10/2025
๐ง๐ค
So tisanaonele or Kumvera Nyimbo ya Jesh ikutuluka mawali by 11:00AM๐
https://youtu.be/jX5c4sLdXuE?si=9sHjqHS_DVLaUA82
Tikuuzeniko ka Story Momwe tinapezela Luso mwa Mnyamata ameneyu mwina Ena nkulimbikitsika ngati Artist Chifukwa taona Ma Artist ambiri timakhala pa changu.
MEGA Sounds Records inayambila ku Nkhata Bay mu Chaka Cha 2021 chamu June pa nthawi imeneyi ndipomwe tinaona kuti Mfanayu Ali ndi Luso Koma akufunika kuphusha kwambiri tidamupanga sign mwa chikhulupiliro chabe kuti tikhoza kumuthandiza nde timamupatsa ma Session aulele by and by timafunabe titamupititsa patali because Luso lake silimayenela kuthela mu Nkhata Bay Mokha nde timaphusha pang'ono pang'ono ngakhale naye amaona Kuchedwa Koma timamulimbikitsa kuti tadekha zabwino zimatenga Nthawi and the good thing is that naye sanafooke Koma kutikhulupilira kuti we will work things out for him.
Fast forward Lero ndi 2025 ku mapeto and pa 31 October tikutulutsa his first Audio and Video and we are ready to push him mu Malawi and ngati mwayi ulipo Globally
Phunziro: Tiyeni Tidekhe, Tikadekha Zabwino Zimakupeza uli Ready. Zikomo
26/10/2025
๐ฅ๐ฏ Save The Sound and Date
26/10/2025
Kumapempheratu Kumeneko
HAPPY SUNDAY
21/10/2025
Save The Date 31st October 2025 My First Single.. Haatiii Jeeeshiiii๐ฅ๐ฅ๐๏ธ๐๏ธ๐๏ธ
We are so Exited to announce our very first Artist to work with his name is Jesh an AfroBeat Artist from Nkhata Bay, Malawi.
Please Subscribe on Our YouTube Channel on the Link below to save the premiere
https://youtu.be/jX5c4sLdXuE?si=ESI6OFWJmVOwIDkc
20/10/2025
Osaiphonya imeneyi Tiyeni Ku YouTube and Subscribe link munsimu๐๐
https://youtu.be/jX5c4sLdXuE?si=ESI6OFWJmVOwIDkc
Komaso Spotify link ndi iyi ๐๐
https://distrokid.com/hyperfollow/jesh6/wanga-ndiwe
Congratulations to Jesh from Nkhatabay as he is the first artist to be signed under MEGA Sounds Records
Eni ake a Music label, Mr Manda and Rita ati Jesh akulutsa kanema wake oyamba, โWanga Ndiweโ Mwezi uno pa 31st.
โ Mega Sounds Records is ready to work with different creatives in the entertainment industry and sign more artists. Pastani ma artist wa Support โ - Adatelo Mrs Rita Manda atamusayina mnyamatayu
20/10/2025
๐ฅ๐ฅ
Atalengeza kuti akufuna anthu a Luso kuti awathandize kupititsa Luso lawo pa tsogolo ayambapodi
Uyu ndi Jesh waku Nkhata Bay emwe wakhala artist oyamba kupangidwa sign ndi MEGA SOUNDS RECORDS and his new song will drop this month on 31st October
Nkutheka inuso muli ndi Luso lililonse follow MEGA Sounds Records kuti muwafotokozere zomwe mumapangazo zikawasangalasa ayambapo kukuthandizani
18/10/2025
family
THIS MESSAGE IS FOR THE CREATIVE WORD. Share, Like and Comment MEGA Sounds Records Sinyoza mafana Ophusha.
Chonde Amemeni anzathu a Luso abwere pa Mudzi pano maganyu asamawadutse Paja Tizigwira Ntchito ndi aliyense ku Entertainment Industry komaso Ongokondaso Entertainment Industry ya Malawi... Tiyeni Tiphushe Limodzi
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Tel Aviv
106100